song lyrics / Tsar Leo / M'manja Mwanu lyrics  | FRen Français

M'manja Mwanu lyrics

Performers Tsar LeoGwambaJoe Kellz

M'manja Mwanu song lyrics by Tsar Leo official

M'manja Mwanu is a song in English

Zonse zachikondi ndazisiya Mmanja mwanu
Mmene dziko lawilira, asochera ana Anu
Mbuyeee, ndi wa chikondi wanga, mutiunikile
Tisasochere
Kwabwera ma Blesser, ma bestie
Ofunakusokoneza basi.
Pacholuka zochita pa Tiktok
Zibwezi zangolowanso ding dong!
Mbuyeee! Tasamba Mmanja
Mbuyeee!
Can you take the wheel for us?

Hook
Nkhani yathu muilembe ndi manja anu
Tsogolo lathu , tiliyike Mmanja mwanu
Dziko lowolali, ine Ndi wa chikondi wanga
Mbuyeee
Tidziika Mmanja mwanu
Mmanja mwanu
Ambuye
Mmanja mwanu
Tate
Mmanja mwanu
Mbuye
Mmanja mwanu
Tate
‌ verse (Gwamba)
Yo! Ku left Blesser!
Ku right ma yo tiku chaser
Akafuna dola ndima kapemphetsa
Walawa za sugar, chibwezi wathetsa!
Walemba status, "I don't date broke guys"
Ine Mtima kugunda!
Komatu mkazi ndinagwira Ali first year
Kubunda !
Wayamba Life yapa Insta
Akuti mwamuna azitumiza dollar instant
Munthune Ka salary ndii konyema
Koma Tsitsi akufuna ndi la kwa naymar
Nde zikafika this far
Pena umaganiza zongozipha!
mbuye wanga Kodi mukundimva?
CHONDE MKAZI WANGA ASASANDUKE DIVA!!!

‌Hook

Nkhani yathu muilembe ndi manja anu
Tsogolo lathu , tiliyike Mmanja mwanu
Dziko lowolali, ine Ndi wa chikondi wanga
Mbuyeee
Tidziika Mmanja mwanu
Mmanja mwanu
Ambuye
Mmanja mwanu
Tate
Mmanja mwanu
Mbuye
Mmanja mwanu
Tate

Outro
Mmanja mwanu
Mbuyee
Mmanja mwanu
Zonse!
Zonseee
Tasiyaaa
Mmanja mwanu
Lyrics copyright : legal lyrics licensed by Lyricfind.
No unauthorized reproduction of lyric.

Comments for M'manja Mwanu lyrics

Name/Nickname
Comment
Copyright © 2004-2024 NET VADOR - All rights reserved. www.paroles-musique.com/eng/
Member login

Log in or create an account...

Forgot your password ?
OR
REGISTER
Select in the following order :
1| symbol to the right of the padlock
2| symbol to the left of the clock
3| symbol at the top of the eye
grid grid grid
grid grid grid
grid grid grid