paroles de chanson / Tsar Leo parole / M'manja Mwanu lyrics  | ENin English

Paroles de M'manja Mwanu

Interprètes Tsar LeoGwambaJoe Kellz

Paroles de la chanson M'manja Mwanu par Tsar Leo lyrics officiel

M'manja Mwanu est une chanson en Anglais

Zonse zachikondi ndazisiya Mmanja mwanu
Mmene dziko lawilira, asochera ana Anu
Mbuyeee, ndi wa chikondi wanga, mutiunikile
Tisasochere
Kwabwera ma Blesser, ma bestie
Ofunakusokoneza basi.
Pacholuka zochita pa Tiktok
Zibwezi zangolowanso ding dong!
Mbuyeee! Tasamba Mmanja
Mbuyeee!
Can you take the wheel for us?

Hook
Nkhani yathu muilembe ndi manja anu
Tsogolo lathu , tiliyike Mmanja mwanu
Dziko lowolali, ine Ndi wa chikondi wanga
Mbuyeee
Tidziika Mmanja mwanu
Mmanja mwanu
Ambuye
Mmanja mwanu
Tate
Mmanja mwanu
Mbuye
Mmanja mwanu
Tate
‌ verse (Gwamba)
Yo! Ku left Blesser!
Ku right ma yo tiku chaser
Akafuna dola ndima kapemphetsa
Walawa za sugar, chibwezi wathetsa!
Walemba status, "I don't date broke guys"
Ine Mtima kugunda!
Komatu mkazi ndinagwira Ali first year
Kubunda !
Wayamba Life yapa Insta
Akuti mwamuna azitumiza dollar instant
Munthune Ka salary ndii konyema
Koma Tsitsi akufuna ndi la kwa naymar
Nde zikafika this far
Pena umaganiza zongozipha!
mbuye wanga Kodi mukundimva?
CHONDE MKAZI WANGA ASASANDUKE DIVA!!!

‌Hook

Nkhani yathu muilembe ndi manja anu
Tsogolo lathu , tiliyike Mmanja mwanu
Dziko lowolali, ine Ndi wa chikondi wanga
Mbuyeee
Tidziika Mmanja mwanu
Mmanja mwanu
Ambuye
Mmanja mwanu
Tate
Mmanja mwanu
Mbuye
Mmanja mwanu
Tate

Outro
Mmanja mwanu
Mbuyee
Mmanja mwanu
Zonse!
Zonseee
Tasiyaaa
Mmanja mwanu
Droits parole : paroles officielles sous licence Lyricfind respectant le droit d'auteur.
Reproduction des paroles interdite sans autorisation.

Commentaires sur les paroles de M'manja Mwanu

Nom/Pseudo
Commentaire
Copyright © 2004-2024 NET VADOR - Tous droits réservés. www.paroles-musique.com
Connexion membre

Se connecter ou créer un compte...

Mot de passe oublié ?
OU
CREER COMPTE
Sélectionnez dans l'ordre suivant :
1| symbole en bas du casque
2| symbole en bas de la croix
3| symbole en haut du téléviseur
grid grid grid
grid grid grid
grid grid grid