song lyrics / Mellz Kumpanje / Magazi (feat. Yashie The Kid) lyrics  | FRen Français

Magazi (feat. Yashie The Kid) lyrics

Performer Mellz Kumpanje

Magazi (feat. Yashie The Kid) song lyrics by Mellz Kumpanje official

Magazi (feat. Yashie The Kid) is a song in English

Ladies and Gentlemen
Sizonke Neh
Anthu nde mukumagundikatu mmakwalalamu
Lero nde
Iyeeeeh
Rasta Mellz Kumpanje

Uyuyu ndi wanga wanga uyuyu ndi ine ndiziabanja ah
Kumuthoka za khalidwe langa sikuti angandisiye panja
Analipo amzanga ena koma sanawapatse danga ah
Mmm mmm mmm mmm
Nde sindimadanda ah
Aaah aah
Tinanjana magazi aah aah
MAGAZI MAGAZI MAGAZI
Aaah aaah tinayanjana magazi aah aah
MAGAZI MAGAZI MAGAZI MAGAZI

Koma nthawi muli nayo eh
Mpaka munayamba kundijeda
Vuto amene mumamungonezayo
Amanditenga ngati breda
Panopano anaiwala zoti iye ndi ine tiku dater
Mumafulumila kukamuthoka koma mumakhala mukuchedwa
Mukamati amuna ako ndi agulu
Amati eya ndine admin
Ndiponso ndimalemba register ya onse ma slay queen
Nde mukuchedwa mukuzizunza
Inu mukungozithera mpweya
Simungathetse
Simungatigwetse
Mungozivuta nkutitchera
Uyuyu ndi wanga wanga uyuyu ndi ine ndiziabanja ah
Kumuthoka za khalidwe langa sikuti angandisiye panja
Analipo amzanga ena koma sanawapatse danga ah
Mmm mmm mmm mmm
Nde sindimadanda ah
Aaah aah
Tinanjana magazi aah aah
MAGAZI MAGAZI MAGAZI
Aaah aaah tinayanjana magazi aah aah
MAGAZI MAGAZI MAGAZI MAGAZI

Iweee
Tinayanjana magazi ife nde nde nde DNA
Olo mutamathoka Trash
Ndikuti sangandisiye ine
Chikondi chaku Mangochi
Blah Blah Tili CHENENE
Nkazangoipondano fada wina nzamuchosa chimbenene
Ndiye
Olo muzimuthoka zimangolowa kutulukira uku
Tinaiphula kale kale sungabudhule za gulu budhu
Muli ndi nthawi mmm mmmh
Ubwino wake kuno chilichonse chili Gudu
Mukhaula chakachino simutitchaisana
Si ife ndudu
Eeeeeeeeh THIRA IWE THIRAAAAA
Inde ndiwathira faya
Ndingompeza master oyambisayo
Sinanga anthuwa ndi choir
Ndikangoti Gwi Gwi Gwi
Ndizamugulira bhawa
Kuti alezere
Avaye
Akanene zina mawa

Uyuyu ndi wanga wanga uyuyu ndi ine ndiziabanja ah
Kumuthoka za khalidwe langa sikuti angandisiye panja
Analipo amzanga ena koma sanawapatse danga ah
Mmm mmm mmm mmm
Nde sindimadanda ah
Aaah aah
Tinanjana magazi aah aah
MAGAZI MAGAZI MAGAZI
Aaah aaah tinayanjana magazi aah aah
Mmmh
MAGAZI MAGAZI MAGAZI MAGAZI

Aaah aaah tinayanjana magazi aah aah
Mmmh
MAGAZI MAGAZI MAGAZI MAGAZI
Lyrics copyright : legal lyrics licensed by Lyricfind.
No unauthorized reproduction of lyric.
Writer: Mellanie Msumba
Copyright: O/B/O DistroKid

Comments for Magazi (feat. Yashie The Kid) lyrics

Name/Nickname
Comment
Copyright © 2004-2024 NET VADOR - All rights reserved. www.paroles-musique.com/eng/
Member login

Log in or create an account...

Forgot your password ?
OR
REGISTER
Select in the following order :
1| symbol to the left of the target
2| symbol to the right of the television
3| symbol at the bottom of magnifying glass
grid grid grid
grid grid grid
grid grid grid