song lyrics / MADALITSO BANDA VOCALIST / CHIKONDI CHA YESU lyrics  | FRen Français

CHIKONDI CHA YESU lyrics

Performer MADALITSO BANDA VOCALIST

CHIKONDI CHA YESU song lyrics by MADALITSO BANDA VOCALIST official

CHIKONDI CHA YESU is a song in English

AaaaaHHH! Eyi Eh Eyi EH!
OoooH Omama!! Chindigometsa Chikondi

Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu
Chikondi cha Yesu ndi chokoma
Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu
Chikondi cha Yesu ndi chokoma

Anachoka mwamba kusiya ulemelero
Kudzafera ife wabwino Yesu
Chikondi chotere ndani akadaonetsa
Koma Yesu adakondetsetsa ife
Kupereka moyo wake kumvera kuwawa Yesu
Koma Yesu akonda ife eeh- aah
Ngati tili m'fulu leroli alipo anamvera kuwawa
ndim'nkondetsetsa poti iye akonda ifeeee!

Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu
Chikondi cha Yesu ndi chokoma
Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu
Chikondi cha Yesu ndi chokoma
Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu
Chikondi cha Yesu ndi chokoma
Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu
Chikondi cha Yesu ndi chokoma

Ooh aaah! NDdichokoma, ndichokoma.
Chatipezetsa moyo aah!

Dziko litachimwa Yesu anasiya zonse
Kumwamba Kudzatifera wabwino Yesu
Kulolera kusiya zonse kudzaombola iwe nd'ne
M'bale mvetsera Yesu atikonda
Ah! Yesu koma a Yesuyo, mundikondera chani ine?
Ndimachimwa kulowa njira zosalungama
Koma a Yesu chikondi chanu pa Ine chiyimabe

Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu
Chikondi cha Yesu ndi chokoma
Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu
Chikondi cha Yesu ndi chokoma
Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu
Chikondi cha Yesu ndi chokoma
Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu
Chikondi cha Yesu ndi chokoma

Chikondi cha Yesu (Chikondano chake)
Chikondi cha Yesu (Chikondano chake)
Chikondi cha Yesu ndi chokoma
Lyrics copyright : legal lyrics licensed by Lyricfind.
No unauthorized reproduction of lyric.
Writer: MADALITSO VOCALIST
Copyright: O/B/O DistroKid

Comments for CHIKONDI CHA YESU lyrics

Name/Nickname
Comment
Copyright © 2004-2024 NET VADOR - All rights reserved. www.paroles-musique.com/eng/
Member login

Log in or create an account...

Forgot your password ?
OR
REGISTER
Select in the following order :
1| symbol at the top of the television
2| symbol at the bottom of the trash
3| symbol to the right of the suitcase
grid grid grid
grid grid grid
grid grid grid